Aroma 8 v 5 to 6)

COMPUTURER REPAIRS AND PHONE
tnm_12_02

Aroma 8 v 5 to 6)
Pakuti Iwo amene Ali monga mwa thupi, asamalira zinthu za thupi, koma Iwo amene ali monga mwa Mzimu,asamalira zinthu za Mzimu. 6.Pakuti chisamaliro cha thupi chili imfa koma cha Mzimu chiri Moyo ndi mtendere.
Wokondedwa Atumiki A Mulungu tiyeni tonse titumikire Mulungu wa Mphamvu zonse, popedza Iye ndi Moyo wathu, ndipo tikuyenera kumutumikira Mulungu nthawi zonse, mu uzimu ndiponso muchoonadi.
Wokondedwa, tiyeni tipewe kuchita zinthu zotsangalatsa thupi, chifukwa nthawi zambiri zinthu zimene zimatsangalatsa thupi ndizimene zimatichimwitsa ndipo Mulungu amadana ndi tchimo nthawi zonse.
Ambuye akudalitseni nonse ndipo adalitsetso Mau ake opatsa Moyo.
Amen.

Nyamata wina anthu ankangomuona ngat osowa zochita

COMPUTURER REPAIRS AND PHONE
tnm_12_02

Nyamata wina anthu ankangomuona ngat osowa zochita, Malinga nkut iyeyo anangonyamuka kwao kumakakhala kwa mfumu basi kumagwira ntchito zapakhomo kumaipelekeza mfumu kumaulendo osiyana siyana.

Azizanke ena ankamufunsa kut
“kodi unaganiza bwanji kumakhala ngat kapolo ku banja lachifumu kumakutuma momwe angafunire”?
Koma iye poyankha amangoti “ZILIBWINO”.

Matsiku akupita choncho, tsiku lina anali paulendo ndi mfumu ndipo mfumu inateleleka nigwa ndipo iye anathamanga nagwira mfumuyi nkuizusa koma anati “ZILIBWINO” mau awawa mfumuyi inanyasidwa nao chifukwa inali kumva ululu mot anakhala kaye kupumulira…

Atangonyamuka anapeza anthu apha galu wachiwewe chakumene yemwe amangoluma aliyense pamseu umenewu ndipo mfumu inaziwa kut akanapanda kugwa akanalumidwa ndithu….anapita ndipo anabwerako.

Tsiku lina ananyamukanso awiri kupita kuuzimba ndipo ntchito yosaka ili nkati kumene kunachoka nguluwe sikunaoneke kut igwire mfumu ija zinakanika malo mwake inaluma chala chamfumu nkuduliratu ndipo nyamata uja ataona anat “ZILIBWINO”

Apapa mfumuyi sinachitire mwina koma kukaika ndende nyamata opanda ulemuyo, sopano inkayenda yokha. Tsiku lina mfumuyi ikuyenda mkhalango, inakumana ndi anthu, akut ankasaka nyama iliyonse kut akachitire nsembe monga mwa chikhalidwe chawo, kaamba koti sanapeze kanthu ,anagwira mfumuyi ulendo nao kut akachitile mwambo wakwawo…..

Atafika ntchito inayambika yoti aphe mfumu koma alimkat anapeza kut mfumuyi ilibe chala chimoz ndipo anat aaaaaaa basi musiyeni munthuyi poti ndi olumala, paja nsembe yathu tikufuna nyama yosalumala…

Pamenepo mfumu ija inasiidwa nipita ndipo inaganizira kut inachita choipa kuika nyamata uja ndende, tsiku inadulidwa chala chija zinalidi bwino akanapanda kutero bwez ataphedwa….

Atafika anamutulusa nyamata uja namupepesa ndi ndalama akatundu ndipo inamulongosolera zonse ndipo nyamatayi anati “ZILIBWINO” Mfumuyi inadabwa, ndipo inat, iwe ndakusunga ndende ndiye ukut zilibwino? Nyamata anati eyatu “ZILIBWINO” mukanapanda kundiika ndende nkanakhala nanu, mene anapeza kut ndiinu olumala akanapha ine poti ndinali osalumala ndipo mfumu inakhala pheeeeee kumapeto kwake Mfumu inati “ZILIBWINO”
Abale wanga kumeneko ndikukuuza kuti ZILIBWINO.
Mulungu potilenga anati ZILIBWINO…. Ndipo nyengo zonse timadusa zabwino kaya zoipa tiyeni tiziziwa kut ZILIBWINO… Ku MIYAMBO akuti KUDYA NYAMA PALI PHOKOSO ZISIYANA NDIKUDYA MASAMBA ULI NDI MTENDERE.
Zinaz osamangotsilira anthu ambiriwa owoneka ngt zikuyenda alibe mtendere wamumtima ndukuuzan sizilibwino tulo lomweli limachita kusowa, vomeleza nyengo zomwe uli ndikumuuza Mulungu kut ZILIBWINO.
Ena ali kuchipatala zokudya zapamwamba zonse zofunika koma akulephera kukhala monga iwe ndiine tachitilamu, M’bale ndi mlongo iwe moyo okhau ukhoza kunena kut ZILIBWINO.
Mulungu akamakusekera khomo amakhala kut akukusegulira lina lachipambano… Mulungu sangalole ntchito yako izitha asanakukonzere ina, sangalole ukhale mumavuto asanakonze mtendere wako… Mavuto enawo amangokhala otipulumutsa kuchivuto chomwe chikanatha kuchosa moyo wathu tiyeni tizingomukhulupirira nthawi zonse.

Nkhani zamasewero ampira mwapatali patali

Precious Sambani of Malawi celebrates goal teammates during the 2018 COSAFA match between Malawi and Botswana at Seshego Stadium, Polokwane on 30 May 2018 ©Samuel Shivambu/BackpagePix

Nkhani zamasewero ampira mwapatali patali
Team ya Malawi the flames ifika mdziko muno mawa loweluka kuchoka ku mpikisano wa Cosafa castle cup omwe ukuchitikira mdziko la South Africa!

COMPUTURER REPAIRS AND PHONE
tnm_12_02

Malawi the Flames yatuluka mu mpikisanowu dzana pamene inafanana mphamvu ndi team ya Botswana 1-1 yoyamba kugoletsa inali Malawi mchigawo choyamba kuchokera kwa Precious Sambani pa 7minutes ndipo Botswana inabweza chigawo chachiwiri nthawi ya ku mapeto zomwe zinakhumudwitsa m’phunzitsi wa team ya dziko lino Rvg komanso amalawi tonse!
Poyankhulapo John Banda yemwe ndi mmodzi osewera wa team ya Flames amene ali nawo mdziko la South Africa iye ndi opepesa pa zomwe timuyi yachita mu mpikisanowu popeza inayamba ndi kugonja ndi Mauritius 1-O ndipo Banda wati ndi zokhumudwitsa kuchinyitsa nthawi yakumapeto ndipo iye wati akudziwa kuti amalawi ndi okhumudwa koma mmalo mwa maplayer anzake John Banda watumiza uthenga opepesa kwa amalawi onse ndipo lero team ya Malawi isewera game yotsiliza ndi team ya Angola nthawi ya 5koloko madzulo!
Kuyankhulapo kwa Ficsher Jahman Kondowe wati ndi okhumudwa momwe timu ya flames yachita mu mpikisano wa Cosafa maka pogonja ndi team ya Mauritius kwa iye anati game ya Mauritius akhoza kusewera opanda training ndi kupambana!
> Team ya Nyasa Big Bullets yapereka contract ya tsopano kwa Katswiri wawo wa pakati Mike Digital Mkwate mpaka 2O2O!
> Nkhani ya chisoni Katswiri wakale wa team ya Prison utd Zomba utd Escom utd komanso Mtl wanderers Innocent Phiri watisiya mmalo mwa Admin anzanga tikungofunira mzimu wa malemu Innocent Phiri kuusa mu mtendere!!!
> Team ya Mighty Beforward wanderers fc yafanana mphamvu 1-1 ndi team ya Namiwawa fc josephy kamwendo anagoletsera Manoma ndipo wanderers ikhale ikubweleranso pa ground kupitiliza zokonzekera zake za mu Superleague pamene akudikira maplayer amene ali ndi team ya flames ku Cosafa cup ndipo iyamba kukhala ndi ma game sabata ikudzayi!!
> Pakadali pa zigoli zokwana 12O ndi zimene zagoletsedwa mu Tnm superleague pa masewero 53 amene aseweledwa mu Tnm kutsatira game ya Silver strikers yomwe inagonjetsa Tn stars 2-1 dzana lachitatu!!
# Nkhani_Za_masewero_za_Kunja !!
> Team ya Black Leopards ya mdziko la south africa yazigulira malo mu League yaikulu ya Absa Priemierleague pamene yagonjetsa Jomo cosmos 1-O mma play offs ake!
Kwa lero pa O1 June 2O18 tisiyane pomwepa tikumane 5koloko pamene tikhale tikukupatsirani sewero la John Chilembwe mu Cosafa cup Malawi vs Angola 5pm

Mai wina adatenga ana ake atatu

COMPUTURER REPAIRS AND PHONE

Mai wina adatenga ana ake atatu napita kukawasia kusukulu monga mwanthwi zonse. Alimunjila adafika pamalo ena pomwe pamaima ma Bus ..
pamenepo adakumana ndimai wina wachikulile yemwe adali ozazidwa ndi nzim wamdyelekezi.
mai wachikulileyo adauza mai wa anayo kuti amupase anawo akamusiile kusukuluko ndipo kamba kanzimu oyipa omwe unamuphimba kumaso mai wa anayu iye adamupatsadi anawo mopanda kumufunsa ngakhale funso limodzi.

tnm_12_02


Apa mai wachikulileyo adawatenga anawo nkuwathawisa ncholinga chokawapha popeleka nsembe kwa mdyelekez wakeyo. Patapita kamphindi mai uja kanzimu kadabwela ndipo adayamba kulila . anthu atamufunsa adafotokoza za maloza omwe amuchitikilawo.
Anthu adasonkhana kuphatikiza achitetezo omwe amayang’anila pamalopo.


Anthuwa adayamba kumusaka mai wakubayo mpaka adakamupeza namugwila .pamene adafikanaye pamalo ochitikila zozizwawo iye adavomelad kuti anawo adawabadi ndicholinga chokawapeleka nsembe.
Apa anthu sadachedwe koma kuyamba kumumenya mai woipayo. atatha kumumenya adamuika mafuta namuotcha monga momwe mukuonelam.

……………
TSopano tawelenga izi
..muzina la Yesu nkhristu ndikubukisa Moto ophyeleza satana kwa inu mukuwelengawe ndi zanja lilonse lomwe likulemba “amen” kuti satana asakhuze ana ako, maloto ako akhale otetezedwa nkati mwa usiku uno, .mudzina la Yesu nkhristu Amen

Akatswiri pankhani za ndale anenetsa kuti

COMPUTURER REPAIRS AND PHONE
tnm_12_02

Akatswiri pankhani za ndale anenetsa kuti zomwe achita aphungu ena achipani cholamula cha DPP pomuwuza mtsogoleri wa dziko lino Peter Mutharika kuti sali kumbali yake ndi chitsimikizo choti nthawi yokakamiza anthu kuti atsate zomwe asakufuna yatha.
Mutharika anayitana aphungu kunyumba ya boma ya Sanjika omwe akhala akubwera poyera kunena kuti Chilima ndiye adzayimire chipani cha DPP pamasankho achaka chamawa.
Anthuwa anakakamizidwa kuti achititse nkumano komwe akanene kuti Mutharika ndiye ayimire chipanichi osati Chilima.
Aphunguwa ndi Patricia Kaliati komaso Noel Masangwi ndi Khansala Louis Ngalande.
Aphunguwa akuti ananenetsa kuti iwo ali kumbali ya Chilima.
Anthuwa akuti anawuzanso Mutharika kuti chipani cha DPP sichingapambane pamasankho pokhapokha iye asiyire Chilima kuti ayimilire chipanichi.

Mkaz wabambo wina waulemu wake ankaopseza mwamuna wakeyo nkumat

COMPUTURER REPAIRS AND PHONE

Mkaz wabambo wina waulemu wake ankaopseza mwamuna wakeyo nkumat achoka pakhomo ati kaamba mwamunayo amaonetsa kuti sakumukonda, inde sakuonetsa chikondi. izitu zinali choncho kaamba koti mkaz yo amatengera zomwe zimachitika kwa aneba awo, iwo nthawi zonse ndipo sanaiwala kumutsekulira mkaz wao chitseko chagalimoto kumbali yomwe wakhala komanso pomwe akufuna kukwera.

Nthawi zambiri mwamunayu amalonjeza kut aziyesesa kutero koma pena amaiwala mpaka mwina kukalowa nyumba pomwe mkaz ali khale m’galimoto kudikira kut mwamuna wake azamutsekulire.
Akatero mkaz amatuluka aliokwiya zedi zimene zimamupasa nkhawa mwamuna ofatsayo.

Tsiku lina mwamuna wankaz yo anapita kukaonana ndi mwamuna neba uja, kuti amufunse chinsinsi chake, kuti amatani kut nthawi zonse asamaiwale kumutsekulira mkaz wake.
Mwamuna nzakeyo atamva izi anatseka mozimvera chitson ndipo anati;
“INEYOTU KUMATSEKULIRA MKAZ WANGA CHITSEKO CHAGALIMOTO SINTENDERE KOMA KUNGOTI CHITSEKO CHAGALIMOTO CHIJA CHOONONGEKA MOTI TIMATSEKULIRA PANJA KOMANSO NDIMACHIDZIWA NDEKHA”

Bambo uja anamva Chisoni ndi mkaz wake kut kaamba kakutsadziwa akutsilira nao zinthu pongozionera patali iye nkumayesa ntendere osaziwa kut anzakewo akuchitira mabvuto.


Mulungu anayankhula kubuku la HOSEYA 4 VS 6 kuti
“ANTHU ANGA SAKUONONGEKA KAAMBA KOTI SATANA ALI KUDZIKO LAPANSI AI, KOMA KAAMBA KAKUSADZIWA”
Anthu kaamba kakutsadziwa talowera moti mpaka wena akutumikira SATANA koma sakudziwa, koma kaamba kongotengera wena poona ngat zikuwayendera naonso anajoina zimenezo osadziwa kut anzao akuchitira mavuto ndipo amalephera kuzituluka.

tnm_12_02

M’bale si oimba GOSPEL onse amene amaimbira zau ufumu wa YEHOVA, ena akungogwiritsidwa ntchito kaamba koti kalero anatengera wena poona ngt akunjoya ali pantendere…komatu Mulungu anati UNDIITANE INE NDIPO NDIZAKUYANKHA IWE NDIKUKUONETSA ZADZIKULU ZOMWE SUZIZIWA.

M’bale ndi Mlongo iwe, usalimbane ndikukangana ndi Mulungu wako nkumaona ngt sakukukonda, usatsilire zomwe akuchita neba poti sudziwa kuti umenewo ndi mtenderedi, zimagalimoto zodula nyumba zapamwamba koma ndukuuza anthu wena utsiku sakugona, usasiye moyo wako m’manja mwa munthu, iweyo paiwe wekha uli ndikuthekera kosintha nyengo zimenezo, gwada pansi mwachikhulupiro ndikuuza Mulungu pemphero la oyera mtima samalisiya choncho.

Peter Mutharika wanenetsa kuti ali ndi umoyo wathanzi ndipo kuti sakudwala.

COMPUTURER REPAIRS AND PHONE
tnm_12_02

Mtsogoleri wadziko lino Peter Mutharika wanenetsa kuti ali ndi umoyo wathanzi ndipo kuti sakudwala.
Izi zikutsatira kanema yemwe akupezeka pa intaneti pomwe Mutharika akuoneka atagwa pamene amalandira mtsogoleri wadziko la Botswana Mokgweetsi Masisi kunyumba yaboma ya Sanjika dzana lapitali.
Mutharika yemwe chaka cha mawa atakwanitse zaka 80 alipampanipani kamba koti anthu ena muchipani chake ati sakumufuna kamba koti wakula ndipo apatse wachiwiri wake Saulos Chilima kuti adzayimilire chipanichi pamasankho omwe achitike chaka chamawa mdziko muno.

Atsogoleri a chipani cha Malawi Congress (MCP) atsimikizira kuti apitiliza kukonzekera nkumano wawo waukulu wa Convention

COMPUTURER REPAIRS AND PHONE
tnm_12_02

Atsogoleri a chipani cha Malawi Congress (MCP) atsimikizira kuti apitiliza kukonzekera nkumano wawo waukulu wa Convention, potsatira chigamulo chomwe bwalo lalikulu la milandu lapereka lero mu mzinda wa Blantyre.
Bwaloli lachotsa chiletso chomwe ena mwa akulu akulu ena a chipanichi anakatenga.
Anthuwa motsogozedwa ndi mlembi wamkulu wa chipanichi Gustav Kaliwo anatenga chiletso kuti msonkhano wa chipanichi usachitike komanso kukana kuyitanidwa ndi utsogoleri wa chipanichi kuti akayankhe mafunso.
Kaliwo pamodzi ndi akulu akulu ena monga Jesse Kabwila, sipikala wa nyumba ya malamulo Richard Msowoya, komanso Tonny Kandiero akhala akudzudzula utsogoleri wa Lazarus Chakwera.

MUNTHU OBADWA NDI MKAZI.

COMPUTURER REPAIRS AND PHONE
tnm_12_02

MUNTHU OBADWA NDI MKAZI.
Munthu obadwa ndi mkazi Ngwa masiku owerengeka, nakhuta mabvuto.
Atuluka ngati duwa , nafota;
Athawa ngati mthuzi osakhalitsa – Yobu 14:1
Abale anga okondedwa, ndi ndani mwa ife yemwe sanabadwe mwa mayi kuti azakhala ndi masiku ochuluka ngati mchenga padziko lino lapasi?
Mlaliki Yobu anayankhula izi ataona kuti anthu anzeru ndi otchuka akumwalira ndi masiku owerengeka.
Yakobo anati kwa Farao, masiku a zaka za moyo wanga ali owerengeka ndi oipa – Gen 47:9.
Ngakhale muli ndi ndalama, chuma, ana, maphunziro, maulamuliro ndi maonekedwe okongola, koma dzindikirani kuti ndinu munthu obadwa ndi mkazi, ndipo masiku anu ndi owerengeka ndi oipa.
Mulungu wakupulumutsani mu zambiri monga ngozi, matenda, nkhondo, ndi muimfa; ndipo ena tinapulumuka mu zipolowe za maiko osiyanasiyana, zonsenzi tinapulumuka ndi mphamvu ya Mulungu osati mwai chabe, nanga tachitapo chani chomuyamika Mulungu wamoyo?
Ndi angati mwa ife amene timapita ku Church kamuyamika Mulungu pa zimene watichitira?
Mtumwi Paulo anati: #Potero_Penyani
_Bwino_umo_muyendera_simonga_opanda_nzeru_kom
a_anzeru_akuchita_machawi_popeza_masiku_ali_oipa! Aefeso 5:15
Mwa ichi anena;
Khala maso ogona iwe , nuuke kwa akufa, ndipo Khristu adzawala pa iwe, Aef 5:14.
Adzawala pa njira yako,
Pa banja lako,
Pantchito pako,
Ndi mumutima mwako.
Amen.