HEALTHY TIPS MACHILITSO AMATENDA OKOZA POGONA🍃🌴

COMPUTURER REPAIRS AND PHONE

HEALTHY TIPS

MACHILITSO AMATENDA OKOZA POGONA🍃🌴

Cinnamon powder ndi njira imodzi yolesera mwana kukoza pogona usiku.paseni mwana wanu chew piece ya cinnamon stick thoroughly once a day.
🌴🍃Apple Cider vinegar🍃🌴
Ikani Apple cider vinegar maspoon awiri mu cup ya madzi azimwa at least katatu PA siku,.
🌴🍃HONEY🍃🌴
Paseni mwana wanu table spoon ya uchi usiku ulionse ,muthanso kuika table spoon yauchi mu cup yake ya mkaka,instead of sugar, to cure the ailment.

tnm_12_02

🌴🍃WALNUTS AND RAISINGS🍃🌴

Patseni mwana wanu 2 walnuts ndi 5 raisins asanapite kokagona
🌴🍃CRANBERRY JUICE🍃🌴
Cranberry juice ndiwabwino kwa bladder and urinary tract, mutha kupasa juice ameneyi chama 4 or 3 PM kuti asazuzike naye kukozakoza.before going to bed.
🌴🍃Kwalero pa topic imeneyi tilekere mpopa koma kuonjezera ndemanga mafuso ndizolandilidwa muthawi ino ZIKOMO🍃🌴

Leave a comment

Leave a Reply

Be the first to comment on "HEALTHY TIPS MACHILITSO AMATENDA OKOZA POGONA🍃🌴"

Leave a comment

Your email address will not be published.


*


");pageTracker._trackPageview();
%d bloggers like this: